Isaiah 21:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mlondayo adafuula kuti, “Ambuye, usana wonse ndimakhala pa nsanja, usiku wonse ndimakhala pa malo anga olondera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anafuulitsa ngati mkango, Ambuye inu, ine ndiimabe pamwamba pa nsanja nthawi ya usana, ndipo ndiikidwa mu ulonda wanga usiku wonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mlondayo anafuwula kuti, “Ambuye anga, tsiku ndi tsiku ndimakhala pa nsanja yolondera; Usiku uliwonse ndimakhala pa malo anga olondera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anapfuulitsa ngati mkango, Ambuye inu, ine ndiimabe pamwamba pa nsanja nthawi ya usana, ndipo ndiikidwa mu ulonda wanga usiku wonse;