Isaiah 22:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawu ulosi wonena za chigwa chooneramo zinthu m'masomphenya: Kodi chachitika nchiyani kuti nonse mukwere pa madenga?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Katundu wa chigwa cha masomphenya. Mwatani kuti mwakwera nonsenu pamachindwi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga wonena za Chigwa cha Masomphenya: Kodi chachitika nʼchiyani, kuti nonsenu mukwere pa madenga?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Katundu wa cigwa ca masomphenya. Mwatani kuti mwakwera nonsenu pamacindwi?