Isaiah 22:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo Ambuye, Chauta Wamphamvuzonse, adakuitanani kuti mulire ndi kudza misozi, kumeta ndi kuvala ziguduli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsiku limenelo Ambuye, Yehova wa makamu, anaitana kulira, ndi kugwa misozi, ndi kumeta, ndi kuvala chiguduli m'chuuno;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku limenelo, Ambuye Yehova Wamphamvuzonse anakuyitanani kuti mulire ndi kukhetsa misozi; kumeta mutu wanu mpala ndi kuvala ziguduli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsiku limenelo Ambuye, Yehova wa makamu, anaitana kulira, ndi kugwa misozi, ndi kumeta, ndi kubvala ciguduli m'cuuno;