Isaiah 22:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye, Chauta Wamphamvuzonse, adandiwuza kuti ndipite kwa Sebina, kapitao woyang'anira nyumba yaufumu, kukamufunsa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova wa makamu, Muka, pita iwe kwa kapitao uyu, kwa Sebina woyang'anira nyumba, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimene Ambuye, Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Pita, ukanene kwa Sabina kapitawo, amene amayangʼanira nyumba yaufumu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova wa makamu, Muka, pita iwe kwa kapitao uyu, kwa Sebina woyang'anira nyumba, ndi kuti,