Isaiah 22:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi ukuchita chiyani kuno? Walimba mtima bwanji kuti udzikumbire manda kuno, kudzikumbira manda pa phiri, ndi kudzisemera mopumulira m'thanthwe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uchitanji iwe kuno, ndimo ndani ali nawe kuno, kuti iwe wagoba manda kuno, ndi kudzigobera manda pamwamba, ndi kudzisemera mogonamo m'thanthwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ukuchita chiyani kuno, nanga ndani anakupatsa chilolezo kuti udzikumbire manda kuno, kudzikumbira manda pa phiri ndi kudzisemera malo opumulira mʼthanthwe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ucitanji iwe kuno, ndimo ndani ali nawe kuno, kuti iwe wagoba manda kuno, ndi kudzigobera manda pamwamba, ndi kudzisemera mogonamo m'thanthwe.