Isaiah 22:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzakugwira dzolimba ndi kukuponya mwamphamvu, iweyo wanyongawe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona Yehova adzakuponya iwe zolimba, monga mwamuna wamphamvu, inde adzakufumbata zolimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Samalira, Yehova watsala pangʼono kukugwira zolimba ndi kukuponya mwamphamvu, iwe munthu wamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona Yehova adzakuponya iwe zolimba, monga mwamuna wamphamvu, inde adzakufumbata zolimba.