Isaiah 22:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adauza Sebina kuti, “Tsiku limenelo ndidzaitana mtumiki wanga Eliyakimu, mwana wa Hilikiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala tsiku limenelo, kuti Ine ndidzaitana mtumiki wanga, Eliyakimu mwana wa Hilikiya:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku limenelo ndidzayitanitsa mtumiki wanga, Eliyakimu mwana wa Hilikiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala tsiku limenelo, kuti ine ndidzaitana mtumiki wanga, Eliakimu mwana wa Hilikiya: