Isaiah 22:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ana ndi adzukulu ake adzakhala katundu wolemera pa iye m'banja la atate ake, monga ngati ziŵiya zonse zimene zimapachikidwa pa chikhomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo adzapachika pa iye ulemerero wonse wa banja la atate wake, obadwa ndi ana, mbiya zonse zazing'ono, ngakhale zikho ndi aguda omwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana ndi abale a nyumba ya abambo ake adzakhala ngati katundu pa iye ngati ziwiya zopanda ntchito zimene zapachikidwa pa chikhomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo adzapacika pa iye ulemerero wonse wa banja la atate wace, obadwa ndi ana, mbiya zonse zazing'ono, ngakhale zikho ndi aguda omwe.