Isaiah 22:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zonse zoteteza Yuda zidalandidwa. Tsiku limenelo mudayang'ana ku zida zankhondo zimene zinali m'Nyumba ya Nkhalango ija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anachotsa chophimba cha Yuda; ndipo iwe unayang'ana tsiku limenelo pa zida za m'nyumba ya nkhalango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zonse zoteteza Yuda zachotsedwa. Ndipo tsiku limenelo munayangʼanayangʼana zida zankhondo zomwe zinali mʼnyumba yaufumu ya nkhalango;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anacotsa cophimba ca Yuda; ndipo iwe unayang'ana tsiku limenelo pa zida za m'nyumba ya nkhalango.