Isaiah 22:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudapeza malo ena m'makoma a mzinda wa Yerusalemu ali ogumuka. Mudasunga madzi m'chidziŵe chakunsi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inu munaona kuti pa mudzi wa Davide panagumuka mipata yambiri; ndipo munasonkhanitsa pamodzi madzi a m'thamanda lakunsi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inu munaona kuti makoma ambiri a mzinda wa Davide anali ndi malo ambiri ogumuka; munasunga madzi mu chidziwe chakumunsi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inu munaona kuti pa mudzi wa Davide panagumuka mipata yambiri; ndipo munasonkhanitsa pamodzi madzi a m'thamanda lakunsi.