Isaiah 23:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mubalalike m'dziko mwanu ngati mtsinje wa Nailo, inu anthu a ku Tarisisi. Palibenso china choti nkukutchinjirizani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pita pakati pa dziko lako monga Nailo, iwe mwana wamkazi wa Tarisisi; palibenso lamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mubalalike mʼdziko mwanu ngati mtsinje wa Nailo inu anthu a ku Tarisisi, pakuti mulibenso chokutetezani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pita pakati pa dziko lako monga Nile, iwe mwana wamkazi wa Tarisi; palibenso lamba.