Isaiah 23:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta watambalitsa dzanja lake kuloza nyanja ndipo wagwedeza maufumu. Walamula a ku Kanani kuti agwetse malinga ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye watambasula dzanja lake panyanja, wagwedeza maufumu; Yehova walamulira Kanani za amalonda, kupasula malinga ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova watambasula dzanja lake kuloza ku nyanja ndipo wagwedeza maufumu ake. Iye walamula kuti Kanaani agwetse malinga ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye watambasula dzanja lace panyanja, wagwedeza maufumu; Yehova walamulira za amalonda, kupasula malinga ace.