Isaiah 23:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lirani kwambiri, inu oyendetsa zombo a ku Tarisisi, chifukwa mzinda wanu wamalinga wagwetsedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuwani, inu ngalawa za Tarisisi; pakuti linga lanu lapasulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lirani mofuwula, inu anthu oyendetsa sitima za pa madzi za ku Tarisisi; chifukwa malinga ako agwetsedwa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuwani, inu ngalawa za Tarisi; pakuti linga lanu lapasulidwa.