Isaiah 23:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tenga zeze wako, uzungulire mzinda, iwe mkazi wachiwerewere woiŵalika. Uimbe zezeyo mokometsera, uimbenso nyimbo zako zija, kuti anthu akukumbukire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tenga mngoli, yendayenda m'mudzi, iwe mkazi wadama, amene unaiwalika; imba zokoma, chulukitsa nyimbo, kuti ukumbukiridwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tenga zeze wako uzungulire mzinda, iwe mkazi wachiwerewere woyiwalika; imba zeze mokometsera, imba nyimbo zambiri, kuti anthu akukumbukire.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tenga mngoli, yendayenda m'mudzi, iwe mkazi wadama, amene unaiwalika; yimba zokoma, curukitsa nyimbo, kuti ukumbukiridwe.