Isaiah 23:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phindu lanu linali tirigu wa ku Sihore, zokolola za ku Nailo, ndipo munkachita malonda ndi anthu a mitundu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa nyanja zazikulu anapindula ndi mbeu za ku Sihori ndizo dzinthu za ku Nailo; ndi kumeneko kunali msika wa amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nyanja zazikulu panabwera tirigu wa ku Sihori; zokolola za ku Nailo, ndipo munachita malonda ndi anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa nyanja zazikuru anapindula ndi mbeu za ku Sihori ndizo dzinthu za ku Nile; ndi kumeneko kunali msika wa amitundu.