Isaiah 23:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aejipito adzadzidzimuka ndi kuchita mantha, akadzamva kuti Tiro adaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pofika mbiriyo ku Ejipito, iwo adzamva kuwawa kwambiri pa mbiri ya Tiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawuwa akadzamveka ku Igupto, iwo adzachita mantha akadzamva kuti Turo wawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pofika mbiriyo ku Aigupto, iwo adzamva kuwawa kwambiri pa mbiri ya Turo.