Isaiah 23:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thaŵirani ku Tarisisi, fuulani mwachisoni, inu okhala m'mphepete mwa nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Olokani inu, kunka ku Tarisisi, kuwani, inu okhala m'chisumbu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolokerani ku Tarisisi, lirani mofuwula, inu anthu okhala mʼmbali mwa nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Olokani inu, kunka ku Tarisi, kuwani, inu okhala m'cisumbu.