Isaiah 23:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndi uwu mzinda wa Tiro wotchukawu, mzinda wakalekale uja? Kodi ndi uwu mzinda uja unkatumiza anthu kuwoloka nyanja kukakhala ku maiko ena?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi umene ndi mudzi wanu wokondwa, wachikhalire kale lomwe, umene mapazi ake anaunyamula kunka nao kutali kukhalako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi uwu si mzinda wachisangalalo uja, mzinda wakalekale, umene anthu ake ankapita kukakhala ku mayiko akutali?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi umene ndi mudzi wanu wokondwa, wacikhalire kale lomwe, umene mapazi ace anaunyamula kunka nao kutari kukhalako?