Isaiah 23:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndani amene adakonza zimenezi kuti zigwere Tiro, mzinda uja wopereka ukulu kwa anthuwu, umene amalonda ake anali akalonga ndiponso otchuka kwambiri pa dziko lonse lapansi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani wapanga uphungu uno pa Tiro, mudzi umene upereka akorona, amalonda ake ali akalonga, ogulitsa ake ali olemekezeka pa dziko lapansi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani anakonza zimenezi kuti zigwere Turo, mzinda umene unakhazikitsa mizinda ina, mzinda umene amalonda ake ndi akalonga ndi otchuka pa dziko lapansi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani wapanga uphungu uno pa Turo, mudzi umene upereka akorona, amalonda ace ali akalonga, ogulitsa ace ali olemekezeka pa dziko lapansi?