Isaiah 24:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoona, Chauta adzaononga dziko lapansi ndi kulisandutsa chipululu. Adzalisakaza, nadzamwaza anthu ake onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Yehova apululutsa dziko, nalipasula, nalitembenuza dodolido, nabalalitsa okhalamo ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, Yehova adzawononga dziko lapansi ndi kulisandutsa chipululu; Iye adzasakaza maonekedwe ake ndi kumwaza anthu ake onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Yehova apululutsa dziko, nalipasula, nalitembenuza dodolido, nabalalitsa okhalamo ace.