Isaiah 24:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu akufuula m'miseu chifukwa cha kusoŵa kwa vinyo. Chimwemwe chonse chatheratu, palibenso chisangalalo pa dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muli mfuu m'makwalala chifukwa cha vinyo; kukondwa konse kwadetsedwa, kusangalala kwa dziko kwatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu akulira mʼmisewu kufuna vinyo; chimwemwe chonse chatheratu, palibenso chisangalalo pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muli mpfuu m'makwalala cifukwa ca vinyo; kukondwa konse kwadetsedwa, kusangalala kwa dziko kwatha.