Isaiah 24:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda wasanduka bwinja, zipata zake zagumuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mudzi mwatsala bwinja, ndi chipata chamenyedwa ndi chipasuko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mzinda wasanduka bwinja zipata zake zagumuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mudzi mwatsala bwinja, ndi cipata camenyedwa ndi cipasuko.