Isaiah 24:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu anthu a dziko lapansi, zoopsa, mbuna ndi misampha zikukudikirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mantha ndi dzenje ndi msampha zili pa iwe, wokhala m'dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu anthu adziko lapansi, zoopsa, dzenje ndi msampha zikukudikirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mantha ndi dzenje ndi msampha ziri pa iwe, wokhala m'dziko.