Isaiah 24:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo Chauta adzalanga kumwamba zamphamvu zakumwamba, ndipo pansi pano mafumu a pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzali tsiku limenelo, kuti Yehova adzazonda kumwamba khamu lakumwamba, ndi mafumu a dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limenelo Yehova adzalanga amphamvu a kumwamba ndiponso mafumu apansi pano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzali tsiku limenelo, kuti Yehova adzazonda kumwamba khamu la kumwamba, ndi mafumu a dziko lapansi.