Isaiah 24:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lapansi lidzaonongedwa kwathunthu, lidzasakazikiratu, pakuti Chauta wanena zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lidzapululuka konse, ndi kupasulidwa ndithu; pakuti Yehova anenana mau amenewa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lapansi lidzawonongedwa kwathunthu ndi kusakazikiratu. Yehova wanena mawu awa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lidzapululuka konse, ndi kupasulidwa ndithu; pakuti Yehova ananena mau amenewa.