Isaiah 24:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko likulira ndipo likufota. Dziko lonse lapansi likuvutika ndipo likuuma. Mlengalenga ukuvutika pamodzi ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lirira nilifota, dziko lilefuka nilifota, anthu omveka a padziko alefuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lapansi likulira ndipo likufota, dziko lonse likuvutika ndipo likuwuma, anthu omveka a dziko lapansi akuvutika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lilira nilifota, dziko lilefuka nilifota, anthu omveka a padziko alefuka.