Isaiah 24:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kulira kokometsera kwa ting'oma tao kwatha, phokoso la anthu osangalala latha, zeze wosangalatsa uja wati zii.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kusangalala kwa mangaka kwalekeka, phokoso la iwo amene asekera litha, kukondwa kwa mngoli kwalekeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulira kokometsera kwa matambolini kwatha, phokoso la anthu osangalala latha, zeze wosangalatsa wati zii.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kusangalala kwa mangaka kwalekeka, phokoso la iwo amene aserera litha, kukondwa kwa mngoli kwalekeka.