Isaiah 24:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu saimbanso pomwa vinyo, akamamwa zaukali zimaŵaŵa m'kamwa mwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo sadzamwa vinyo ndi kuimba nyimbo; chakumwa chaukali chidzawawa kwa iwo amene achimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu sadzayimbanso akumwa vinyo; akadzamwa zaukali zidzakhala zowawa mʼkamwa mwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo sadzamwa vinyo ndi kuyimba nyimbo; cakumwa caukali cidzawawa kwa iwo amene acimwa.