Isaiah 25:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda uja mwausandutsa mulu wamiyala, Mzinda wamalinga uja mwausandutsa bwinja. Nyumba zamphamvu za adani athu si mzindanso tsopano, sizidzamangidwanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa Inu mwasandutsa mudzi muunda; mudzi walinga bwinja; nyumba ya alendo kuti isakhale mudzi; sudzamangidwa konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwasandutsa mzinda uja kukhala mulu wamiyala. Ndipo mzinda wamalinga wasanduka bwinja, linga la anthu achilendo lero si mzindanso ndipo sidzamangidwanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa Inu mwasandutsa mudzi muunda; mudzi walinga bwinja; nyumba ya alendo kuti isakhale mudzi; sudzamangidwa konse.