Isaiah 25:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake anthu amphamvu a mitundu yonse adzakutamandani, m'mizinda ya mitundu yankhalwe anthu adzakuwopani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anthu amphamvu adzakulemekezani Inu, mudzi wa mitundu yakuopsa udzakuopani Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake anthu amphamvu adzakulemekezani; mizinda ya mitundu ya anthu ankhanza idzakuopani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anthu amphamvu adzakulemekezani Inu, mudzi wa mitundu yakuopsya udzakuopani Inu.