Isaiah 26:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, pamene anali m'masautso, anthu anu adakufunafunani, pamene munkaŵalanga, adapemphera kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, iwo adza kwa Inu movutika, iwo anathira pemphero, muja munalikuwalanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova, anthu anu anabwera kwa Inu pamene anali mʼmasautso; pamene munawalanga, iwo anapemphera kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, iwo adza kwa Inu mobvutika, iwo anathira pemphero, muja munalikuwalanga.