Isaiah 26:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, mumapatsa mtendere weniweni kwa amene ali ndi mtima wokhazikika, chifukwa chokhulupirira Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu mudzasunga mtima wokhazikika mu mtendere weniweni, chifukwa ukukhulupirirani Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mudzamupatsa munthu wa mtima wokhazikika mtendere weniweni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mudzasunga mtima wokhazikika mu mtendere weni weni, cifukwa ukukhulupirirani Inu.