Isaiah 27:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo Chauta adzalankhula za munda wake wokoma wamphesa. Adzati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku limenelo: munda wa mphesa wavinyo, imbani inu za uwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limenelo Yehova adzati, “Tidzayimba nyimbo ya munda wamphesa wobereka bwino:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku limenelo: munda wa mphesa wavinyo, yimbani inu za uwo.