Isaiah 27:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ine Chauta ndine mlonda wa mundawo, nthaŵi zonse ndimauthirira. Ndimaulonda usana ndi usiku, kuti wina angauwononge.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine Yehova ndiusunga uwo; ndidzauthirira madzi nthawi zonse; ndidzausunga usiku ndi usana, kuti angauipse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine, Yehova, ndimawuyangʼanira; ndimawuthirira nthawi zonse. Ndimawulondera usana ndi usiku kuti wina angawononge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine Yehova ndiusunga uwo; ndidzauthirira madzi nthawi zonse; ndidzausunga usiku ndi usana, kuti angauipse.