Isaiah 27:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindidzaukwiyiranso munda wanga wamphesawo. Minga ndi mkandankhuku zidakati ziwoneke, ndikadalimbana nazo ndi kuzitentha kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilibe ukali; ndani adzalimbanitsa lunguzi ndi minga ndi Ine kunkhondo? Ndiziponde ndizitenthe pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine sindinakwiye. Ngati mkandankhuku ndi minga zikanaoneka ndikanalimbana nazo! Ndikachita nazo nkhondo; ndikanazitentha zonse ndi moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiribe ukali; ndani adzalimbanitsa lunguzi ndi minga ndi Ine kunkhondo? ndiziponde ndizitenthe pamodzi.