Isaiah 27:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Chauta adalanga Aisraele monga m'mene adalangira adani ao? Kodi Aisraele adaphedwa monga m'mene adaphera adani ao?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Mulungu wakantha Yakobo, monga umo anawakanthira akumkanthawo? Kapena kodi iye waphedwa malinga ndi kuphedwa kwa iwo amene anaphedwa ndi iye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Yehova anakantha Israeli ngati momwe anakanthira anthu amene anazunza Israeli? Kapena kodi Yehova anapha Israeli ngati mmene anthu ena anaphera Israeli?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Mulungu wakantha Yakobo, monga umo anawakanthira akumkanthawo? kapena kodi iye waphedwa malinga ndi kuphedwa kwa iwo amene anaphedwa ndi iye?