Isaiah 28:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzakhala ngati munthu wogona pa bedi lalifupi kwambiri, kotero kuti sangatambalitsepo miyendo, ndiponso ngati munthu wofunda kabulangete kopereŵera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kama wafupika, munthu sangatambalale pamenepo; ndi chofunda chachepa, sichingamfikire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakhala ngati munthu wogona pa bedi lalifupi kwambiri kuti sangathe kutambalitsapo miyendo; ndiponso mudzakhala ngati munthu amene wafunda bulangeti lochepa kwambiri kuti sangathe nʼkufunda komwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kama wafupika, munthu sangatambalale pamenepo; ndi copfunda cacepa, sicingamfikire.