Isaiah 28:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mlimi wofuna kubzala amangokhalira kutipula kokhakokha? Kodi amangokhalira kugaula ndi kugalauza?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mlimi amalimabe kuti abzale? Kodi amachocholabe, ndi kuswa zibuma za nthaka?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mlimi wofuna kudzala mbewu amangokhalira kutipula kokhakokha? Kodi amangokhalira kugawula ndi kugalawuza kokhakokha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mlimi amalimabe kuti abzale? kodi amacocolabe, ndi kuswa zibuma za nthaka?