Isaiah 28:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndiye amamulangiza ndi kumphunzitsa njira yokhoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mulungu wake amlangiza bwino namphunzitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wake amamulangiza ndi kumuphunzitsa njira yabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mulungu wace amlangiza bwino namphunzitsa.