Isaiah 28:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maŵere sapuntha poponderezapo ndi gareta lopanda mikombero, ndipo chitoŵe sapuntha popondetsapo mikombero ya gareta. Maŵere amapuntha ndi kamtengo, chitoŵe amaomba ndi ndodo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sapuntha mawere ndi chopunthira chakuthwa, ngakhale kuzunguniza njinga ya galeta pachitowe; koma amakulunga mawere ndi munsi, naomba chitowe ndi chibonga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawere sapunthira chopunthira cha galeta lopanda mikombero, kapena chitowe sapuntha popondetsapo mikombero ya galeta; mawere amapuntha ndi ndodo ndipo chitowe amapuntha ndi kamtengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sapuntha mawere ndi copunthira cakuthwa, ngakhale kuzunguniza njinga ya gareta pacitowe; koma amakulunga mawere ndi munsi, naomba citowe ndi cibonga.