Isaiah 29:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta wakugonetsani tulo tofa nato. Wakutsekani maso, inu aneneri, wakuphimbani kumutu, inu olosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova watsanulira pa inu mzimu wa tulo togonetsa, natseka maso anu, ndiwo aneneri; naphimba mitu yanu, ndiwo alauli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wakugonetsani tulo tofa nato. Watseka maso anu, inu aneneri; waphimba mitu yanu, inu alosi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova watsanulira pa inu mzimu wa tulo togonetsa, natseka maso anu, ndiwo aneneri; naphimba mitu yanu, ndiwo alauli.