Isaiah 29:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati bukulo mupatsa wina wosadziŵa kuŵerenga kuti aŵerenge, adzanena kuti “Sindidziŵa kuŵerenga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo buku laperekedwa kwa wosadziwa kuwerenga, ndi kuti, Werengani umu; koma ati, Ine sindinaphunzira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapena ngati lipatsidwa kwa amene sadziwa kuwerenga ndi kunena kuti, “Chonde werenga bukuli,” iye adzayankha kuti, “Ine sindidziwa kuwerenga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo buku laperekedwa kwa wosadziwa kuwerenga, ndi kuti, Werengani umu; koma ati, Ine sindinaphunzira.