Isaiah 29:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu odzichepetsa adzakhalanso ndi chimwemwe mwa Chauta, ndipo anthu osauka adzakondwa chifukwa cha Woyera uja wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ofatsanso kukondwa kwao kudzachuluka mwa Yehova, ndi aumphawi a mwa anthu adzakondwerera mwa Woyera wa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu odzichepetsa adzakhalanso ndi chimwemwe mwa Yehova; ndipo anthu osowa adzakondwa chifukwa cha Woyerayo wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ofatsanso kukondwa kwao kudzacuruka mwa Yehova, ndi aumphawi a mwa anthu adzakondwerera mwa Woyera wa Israyeli.