Isaiah 29:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamenepo Mulungu adzauthira nkhondo mzinda wa Ariyele. Tsono kudzakhala kulira ndi kudandaula, ndipo mzindawo udzasanduka ng'anjo ya guwa lansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo ndidzasautsa Ariyele, ndipo padzakhala maliro ndi kulira; koma iye adzakhala kwa Ine monga Ariyele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu Ine ndidzathira nkhondo Arieli ndipo kudzakhala kulira ndi kudandaula, mzindawo udzasanduka ngati ngʼanjo ya guwa lansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo ndidzasautsa Arieli, ndipo padzakhala maliro ndi kulira; koma iye adzakhala kwa Ine monga Arieli.