Isaiah 29:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ankhanza adzatheratu, oseka anzao adzazimirira, ndipo opendekera ku zoipa adzaonongedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti woopsa wagoma, ndi wonyoza watha, ndi onse odikira zolakwa alikhidwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu ankhanza adzazimirira, oseka anzawo sadzaonekanso, ndipo onse okopeka ndi zoyipa adzawonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti woopsya wagoma, ndi wonyoza watha, ndi onse odikira zolakwa alikhidwa;