Isaiah 29:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu opusa adzapeza nzeru, onyinyirika adzavomera malangizo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwonso osochera mumzimu adzadziwa luntha, ndi iwo amene ang'ung'udza adzaphunzitsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu opusa adzapeza nzeru; onyinyirika adzalandira malangizo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwonso osocera mumzimu adzadziwa luntha, ndi iwo amene ang'ung'udza adzaphunzitsidwa.