Isaiah 29:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga Davide, Mulungu adzamangako zithando zankhondo zolimbana ndi mzindawo, adzauzinga ndi nsanja zankhondo ndi kumanga mitumbira youthirira nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzamanga zithando kuzungulira iwe ponse, ndipo ndidzamanga linga ndi kuunjika miulu yakumenyanirana ndi iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzamanga misasa ya nkhondo kulimbana ndi mzindawo; ndidzakuzungulira ndi nsanja za nkhondo ndi kumanga mitumbira yanga ya nkhondo kulimbana nawe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzamanga zithando kuzungulira iwe ponse, ndipo ndidzamanga linga ndi kuunjika miulu yakumenyanirana ndi iwe.