Isaiah 29:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudodome ndipo mukhale ozizwa. Dzichititseni khungu ndipo mukhalebe osapenya. Muledzere, koma osati ndi vinyo, ndipo mudzandire, koma osati ndi chakumwa chaukali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khalani ndi kudabwa; sangalalani ndi kukhala akhungu; iwo aledzera, koma si ndi vinyo, ali dzandidzandi; koma si ndi chakumwa chaukali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pitirizani kuledzera ndipo mudzakhala opusa. Dzitsekeni mʼmaso ndipo mukhale osapenya, ledzerani, koma osati ndi vinyo, dzandirani, koma osati ndi mowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khalani ndi kudabwa; sangalalani ndi kukhala akhungu; iwo aledzera, koma si ndi vinyo, ali dzandi dzandi; koma si ndi cakumwa caukali.