Isaiah 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu omvera Mulungu pakuti zinthu zidzaŵayendera bwino, adzakondwera ndi phindu la ntchito zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani za wolungama, kuti kudzamkomera iye; chifukwa oterowo adzadya zipatso za machitidwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nena kwa olungama kuti zonse zidzawayendera bwino, pakuti adzakondwera ndi phindu la ntchito zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani za wolungama, kuti kudzamkomera iye; cifukwa oterowo adzadya zipatso za macitidwe ao.