Isaiah 3:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsoka kwa anthu oipa! Zinthu zidzaŵaipira. Zimene akhala akuchitira anzao zomwezo zidzaŵabwerera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka kwa woipa! Kudzamuipira; chifukwa kuti mphotho ya manja ake idzapatsidwa kwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa anthu oyipa! Mavuto ali pa iwo! Adzalandira malipiro a zimene manja awo anachita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka kwa woipa! kudzamuipira; cifukwa kuti mphotho ya manja ace idzapatsidwa kwa iye.